Machitidwe 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ophunzira ena a ku Kaisareya+ ananyamuka nafe, kuti atiperekeze kunyumba ya munthu wina kuti tikafikire kumeneko. Munthu ameneyu dzina lake linali Mnaso wa ku Kupuro, ndipo anali mmodzi wa ophunzira oyambirira.
16 Koma ophunzira ena a ku Kaisareya+ ananyamuka nafe, kuti atiperekeze kunyumba ya munthu wina kuti tikafikire kumeneko. Munthu ameneyu dzina lake linali Mnaso wa ku Kupuro, ndipo anali mmodzi wa ophunzira oyambirira.