Machitidwe 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mkulu wa asilikaliyo anati: “Ine ndinagula ufulu umenewu wokhala nzika ndi ndalama zambiri.” Paulo anati: “Koma ine wanga ndinachita kubadwa+ nawo.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:28 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 184
28 Mkulu wa asilikaliyo anati: “Ine ndinagula ufulu umenewu wokhala nzika ndi ndalama zambiri.” Paulo anati: “Koma ine wanga ndinachita kubadwa+ nawo.”