Machitidwe 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mawu amodzi okha amene ine ndinafuula, pamene ndinaimirira pakati pawo ndi akuti, ‘Ine lero ndikuweruzidwa pamaso panu chifukwa cha nkhani ya kuuka kwa akufa!’”+
21 Mawu amodzi okha amene ine ndinafuula, pamene ndinaimirira pakati pawo ndi akuti, ‘Ine lero ndikuweruzidwa pamaso panu chifukwa cha nkhani ya kuuka kwa akufa!’”+