Machitidwe 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Paulo anayankha kuti: “Ine ndaimirira kutsogolo kwa mpando woweruzira milandu wa Kaisara,+ kumene ndiyenera kuweruzidwa. Ayuda+ sindinawalakwire chilichonse, monga mmene inunso mukuonera. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:10 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 198 Nsanja ya Olonda,12/15/2001, ptsa. 23-24
10 Paulo anayankha kuti: “Ine ndaimirira kutsogolo kwa mpando woweruzira milandu wa Kaisara,+ kumene ndiyenera kuweruzidwa. Ayuda+ sindinawalakwire chilichonse, monga mmene inunso mukuonera.