Machitidwe 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Fesito ananena kuti: “Mfumu Agiripa ndi anthu nonse amene muli nafe pano, mukumuona munthu uyu. Ayuda onse anandipempha ine ku Yerusalemu komanso kuno, mofuula kuti iyeyu sayeneranso kukhala ndi moyo.+
24 Ndiyeno Fesito ananena kuti: “Mfumu Agiripa ndi anthu nonse amene muli nafe pano, mukumuona munthu uyu. Ayuda onse anandipempha ine ku Yerusalemu komanso kuno, mofuula kuti iyeyu sayeneranso kukhala ndi moyo.+