Machitidwe 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma popeza kuti mphepo yamkuntho inali kutiwomba ndi kutikankha mwamphamvu, tsiku lotsatira anthu anayamba kutaya katundu kuti ngalawa ipepukidwe.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:18 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, tsa. 24
18 Koma popeza kuti mphepo yamkuntho inali kutiwomba ndi kutikankha mwamphamvu, tsiku lotsatira anthu anayamba kutaya katundu kuti ngalawa ipepukidwe.+