-
Machitidwe 28:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma pamene Paulo anatola kamtolo ka nkhuni ndi kukaika pamoto, panatuluka njoka ya mphiri chifukwa cha kutentha ndipo inaluma ndi kukanirira kudzanja la Paulo.
-