Machitidwe 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anali kuyembekezera kuti atupa kapena agwa mwadzidzidzi n’kufa. Koma atayembekezera nthawi yaitali n’kuona kuti palibe choopsa chimene chikumuchitikira, anasintha maganizo awo ndi kuyamba kumunena kuti ndi mulungu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:6 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 210
6 Iwo anali kuyembekezera kuti atupa kapena agwa mwadzidzidzi n’kufa. Koma atayembekezera nthawi yaitali n’kuona kuti palibe choopsa chimene chikumuchitikira, anasintha maganizo awo ndi kuyamba kumunena kuti ndi mulungu.+