Aroma 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chotero, kodi pamenepa palinso chifukwa chodzitama nacho?+ Palibiretu. Malinga ndi chilamulo chiti?+ Chija chofuna ntchito?+ Ndithudi ayi, koma mwa lamulo la chikhulupiriro.+
27 Chotero, kodi pamenepa palinso chifukwa chodzitama nacho?+ Palibiretu. Malinga ndi chilamulo chiti?+ Chija chofuna ntchito?+ Ndithudi ayi, koma mwa lamulo la chikhulupiriro.+