Aroma 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ngati ukulengeza kwa anthu ‘mawu amene ali m’kamwa mwakowo,’+ akuti Yesu ndiye Ambuye,+ ndipo mumtima mwako ukukhulupirira kuti Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ udzapulumuka.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:9 Nsanja ya Olonda,12/15/1997, tsa. 19
9 Pakuti ngati ukulengeza kwa anthu ‘mawu amene ali m’kamwa mwakowo,’+ akuti Yesu ndiye Ambuye,+ ndipo mumtima mwako ukukhulupirira kuti Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ udzapulumuka.+