Aroma 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiponso, ngati mbali ya mtanda imene yadyedwa monga chipatso choyambirira+ ili yoyera, ndiye kuti mtanda wonse ndi woyeranso. Ngati muzu uli woyera,+ ndiye kuti nthambi nazonso ndi zoyera. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:16 Nsanja ya Olonda,5/15/2011, tsa. 23
16 Ndiponso, ngati mbali ya mtanda imene yadyedwa monga chipatso choyambirira+ ili yoyera, ndiye kuti mtanda wonse ndi woyeranso. Ngati muzu uli woyera,+ ndiye kuti nthambi nazonso ndi zoyera.