Aroma 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho taona kukoma mtima+ komanso kusalekerera+ kwa Mulungu. Amene anagwa anaona kusalekerera+ kwake, koma iweyo ukuona kukoma mtima kwa Mulungu, malinga ngati ukukhalabe+ m’kukoma mtima kwake. Apo ayi, iwenso udzadulidwa.+
22 Choncho taona kukoma mtima+ komanso kusalekerera+ kwa Mulungu. Amene anagwa anaona kusalekerera+ kwake, koma iweyo ukuona kukoma mtima kwa Mulungu, malinga ngati ukukhalabe+ m’kukoma mtima kwake. Apo ayi, iwenso udzadulidwa.+