Aroma 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nanga n’chifukwa chiyani umaweruza m’bale wako?+ Kapenanso n’chifukwa chiyani umanyoza m’bale wako? Pakuti tonse tidzaimirira patsogolo pa mpando woweruzira milandu+ wa Mulungu. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:10 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 35 Nsanja ya Olonda,9/1/2004, tsa. 10
10 Nanga n’chifukwa chiyani umaweruza m’bale wako?+ Kapenanso n’chifukwa chiyani umanyoza m’bale wako? Pakuti tonse tidzaimirira patsogolo pa mpando woweruzira milandu+ wa Mulungu.