Aroma 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa chifukwa chimenechi, tisamaweruzane,+ koma m’malomwake tsimikizani mtima+ kuti simuikira m’bale wanu+ chokhumudwitsa+ kapena chopunthwitsa. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:13 Galamukani!,10/8/2005, tsa. 17
13 Pa chifukwa chimenechi, tisamaweruzane,+ koma m’malomwake tsimikizani mtima+ kuti simuikira m’bale wanu+ chokhumudwitsa+ kapena chopunthwitsa.