Aroma 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Siyani kuwononga ntchito ya Mulungu chifukwa cha zakudya basi.+ Zoonadi, zinthu zonse ndi zoyera, koma munthu amene amadya ngakhale pamene akukhumudwitsa ena, amalakwa.+
20 Siyani kuwononga ntchito ya Mulungu chifukwa cha zakudya basi.+ Zoonadi, zinthu zonse ndi zoyera, koma munthu amene amadya ngakhale pamene akukhumudwitsa ena, amalakwa.+