Aroma 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:9 Nsanja ya Olonda,7/1/1997, ptsa. 18-19
9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+