1 Akorinto 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikutanthauza kuti, ena mwa inu amanena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ena amati, “Ine ndine wa Apolo,”+ enanso amati “Ine ndine wa Kefa,” pamene ena amati, “Ine ndine wa Khristu.” 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:12 Nsanja ya Olonda,10/1/1996, ptsa. 21-22
12 Ndikutanthauza kuti, ena mwa inu amanena kuti: “Ine ndine wa Paulo,” ena amati, “Ine ndine wa Apolo,”+ enanso amati “Ine ndine wa Kefa,” pamene ena amati, “Ine ndine wa Khristu.”