1 Akorinto 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikulankhula choncho kuti ndikuchititseni manyazi.+ Kodi zoona palibe wanzeru ndi mmodzi yemwe+ pakati panu amene angaweruze mlandu pakati pa abale ake?
5 Ndikulankhula choncho kuti ndikuchititseni manyazi.+ Kodi zoona palibe wanzeru ndi mmodzi yemwe+ pakati panu amene angaweruze mlandu pakati pa abale ake?