1 Akorinto 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma kwa enawa, ineyo, osati Ambuye,+ ndikunena kuti: Ngati pali m’bale amene ali ndi mkazi wosakhulupirira, ndipo mkaziyo akulola kukhala naye, asamusiye mkaziyo. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:12 Nsanja ya Olonda,10/15/1996, ptsa. 21-22 Kukambitsirana, ptsa. 385-386
12 Koma kwa enawa, ineyo, osati Ambuye,+ ndikunena kuti: Ngati pali m’bale amene ali ndi mkazi wosakhulupirira, ndipo mkaziyo akulola kukhala naye, asamusiye mkaziyo.