1 Akorinto 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano ngati ndikulengeza uthenga wabwino,+ chimenechi si chifukwa chodzitamira, pakuti ndinalamulidwa kutero.+ Ndithudi, tsoka+ kwa ine ngati sindilengeza uthenga wabwino! 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:16 Galamukani!,8/8/2001, tsa. 20 Nsanja ya Olonda,9/15/1996, ptsa. 17-18
16 Tsopano ngati ndikulengeza uthenga wabwino,+ chimenechi si chifukwa chodzitamira, pakuti ndinalamulidwa kutero.+ Ndithudi, tsoka+ kwa ine ngati sindilengeza uthenga wabwino!