1 Akorinto 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kwa ofooka ndinakhala wofooka, kuti ndipindule ofooka.+ Ndakhala zinthu zonse kwa anthu osiyanasiyana,+ kuti mulimonse mmene zingakhalire ndipulumutseko ena. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:22 Nsanja ya Olonda,12/1/2005, ptsa. 27-3111/15/1989, tsa. 12
22 Kwa ofooka ndinakhala wofooka, kuti ndipindule ofooka.+ Ndakhala zinthu zonse kwa anthu osiyanasiyana,+ kuti mulimonse mmene zingakhalire ndipulumutseko ena.