1 Akorinto 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Munthu ayambe wadzifufuza+ ngati ali woyenerera kudya mkatewu ndi kumwa za m’kapuyi. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:28 Nsanja ya Olonda,1/15/2015, ptsa. 15-163/15/1991, ptsa. 21-22