1 Akorinto 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo mbali za thupi zimene timaziona ngati zosalemekezeka kwambiri, n’zimene timazipatsa ulemu wochuluka,+ chotero mbali zathu zosaoneka bwino zimaoneka bwino kwambiri,
23 Ndipo mbali za thupi zimene timaziona ngati zosalemekezeka kwambiri, n’zimene timazipatsa ulemu wochuluka,+ chotero mbali zathu zosaoneka bwino zimaoneka bwino kwambiri,