2 Akorinto 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngati wina wachita kanthu kochititsa chisoni,+ sanachititse chisoni ineyo, koma mwanjira ina wachititsa chisoni nonsenu. Komabe sindikufuna kutsindika mfundo imeneyi mwamphamvu kwambiri.
5 Ngati wina wachita kanthu kochititsa chisoni,+ sanachititse chisoni ineyo, koma mwanjira ina wachititsa chisoni nonsenu. Komabe sindikufuna kutsindika mfundo imeneyi mwamphamvu kwambiri.