23 Koma ngati mukukayikira zilizonse zokhudza Tito, ndikufuna ndikuuzeni kuti iye ndi mnzanga komanso ndikugwira naye ntchito limodzi+ pothandiza inuyo. Kapena ngati mungakayikire zilizonse zokhudza abale athuwa, iwo ndi nthumwi za mipingo ndipo amabweretsa ulemerero kwa Khristu.