2 Akorinto 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndikunena zimenezi mopeputsa ifeyo, ngati kuti ndife ofooka. Koma ngati wina aliyense akuchita chinachake molimba mtima, ndikulankhula ngati wodzitama,+ inenso ndikuchita chinthu chomwecho molimba mtima.
21 Ndikunena zimenezi mopeputsa ifeyo, ngati kuti ndife ofooka. Koma ngati wina aliyense akuchita chinachake molimba mtima, ndikulankhula ngati wodzitama,+ inenso ndikuchita chinthu chomwecho molimba mtima.