Agalatiya 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komabe, ngati ifeyo kapena mngelo wochokera kumwamba angalengeze nkhani ina kwa inu monga uthenga wabwino, koma nkhaniyo n’kukhala yosiyana ndi uthenga wabwino umene tinaulengeza kwa inu, ameneyo akhale wotembereredwa.+
8 Komabe, ngati ifeyo kapena mngelo wochokera kumwamba angalengeze nkhani ina kwa inu monga uthenga wabwino, koma nkhaniyo n’kukhala yosiyana ndi uthenga wabwino umene tinaulengeza kwa inu, ameneyo akhale wotembereredwa.+