Agalatiya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Cholinga chake chinali chakuti mitundu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa kudzera mwa Yesu Khristu,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.+
14 Cholinga chake chinali chakuti mitundu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa kudzera mwa Yesu Khristu,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.+