Agalatiya 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ngakhale zili choncho, kodi Malemba amati chiyani? “Thamangitsani mdzakaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, pakuti sizingatheke mwana wa mdzakazi kudzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wa mkazi waufulu.”+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:30 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 21
30 Ngakhale zili choncho, kodi Malemba amati chiyani? “Thamangitsani mdzakaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, pakuti sizingatheke mwana wa mdzakazi kudzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wa mkazi waufulu.”+