Aefeso 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chinsinsi chimenechi n’chakuti anthu a mitundu ina nawonso akhale odzalandira cholowa, ndipo akhalenso ziwalo za thupi+ ndiponso otenga nawo mbali m’lonjezo pamodzi ndi ife,+ mogwirizana ndi Khristu Yesu kudzera mwa uthenga wabwino. Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:6 Nsanja ya Olonda,2/15/2006, tsa. 19
6 Chinsinsi chimenechi n’chakuti anthu a mitundu ina nawonso akhale odzalandira cholowa, ndipo akhalenso ziwalo za thupi+ ndiponso otenga nawo mbali m’lonjezo pamodzi ndi ife,+ mogwirizana ndi Khristu Yesu kudzera mwa uthenga wabwino.