Aefeso 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho, ndikunena izi ndi kuzichitira umboni mwa Ambuye, kuti musamayendenso monga mmene anthu a mitundu ina+ amayendera, potsatira maganizo awo opanda pake.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:17 Nsanja ya Olonda,3/1/1993, ptsa. 8-10
17 Choncho, ndikunena izi ndi kuzichitira umboni mwa Ambuye, kuti musamayendenso monga mmene anthu a mitundu ina+ amayendera, potsatira maganizo awo opanda pake.+