2 Timoteyo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma tsopano izi zatsimikizirika bwino chifukwa cha kuonekera+ kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu, amene wathetsa mphamvu imfa.+ Kudzera mu uthenga wabwino,+ iye watidziwitsa bwinobwino+ mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+
10 Koma tsopano izi zatsimikizirika bwino chifukwa cha kuonekera+ kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu, amene wathetsa mphamvu imfa.+ Kudzera mu uthenga wabwino,+ iye watidziwitsa bwinobwino+ mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+