2 Timoteyo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Uthenga wabwino umenewu ndi umene anandiikira kuti ndikhale mlaliki, mtumwi ndi mphunzitsi.+