2 Timoteyo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Luka yekha ndiye amene ali ndi ine. Pobwera utengenso Maliko, pakuti iye ndi wofunika kwa ine chifukwa amandithandiza+ pa utumiki wanga. 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 118 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, ptsa. 8-911/15/2007, tsa. 18
11 Luka yekha ndiye amene ali ndi ine. Pobwera utengenso Maliko, pakuti iye ndi wofunika kwa ine chifukwa amandithandiza+ pa utumiki wanga.