Aheberi 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nanga kodi analumbirira+ ndani kuti sadzalowa mu mpumulo wake? Kodi si omwe aja amene anachita zosamvera?+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:18 Nsanja ya Olonda,7/15/1998, tsa. 17
18 Nanga kodi analumbirira+ ndani kuti sadzalowa mu mpumulo wake? Kodi si omwe aja amene anachita zosamvera?+