7 Koma m’chipinda chachiwiricho, mkulu wa ansembe yekha ndiye anali kulowamo kamodzi pa chaka,+ ndipo sanali kulowamo popanda kutenga magazi.+ Magaziwo anali kuwapereka chifukwa cha iye mwini,+ komanso chifukwa cha machimo a anthu amene anachita mosadziwa.+