Yakobo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ngati inu mukutsatira lamulo lachifumu+ lakuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha,”+ monga mmene lemba limanenera, mukuchita bwino ndithu. Yakobo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,5/1/2006, ptsa. 29-3011/15/1997, tsa. 14
8 Tsopano ngati inu mukutsatira lamulo lachifumu+ lakuti: “Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha,”+ monga mmene lemba limanenera, mukuchita bwino ndithu.