1 Petulo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu. 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:25 Nsanja ya Olonda,7/1/1992, tsa. 16
25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.