1 Yohane 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati wina amanena kuti: “Ndimakonda Mulungu,” koma amadana ndi m’bale wake, ndiye kuti ndi wabodza.+ Pakuti amene sakonda m’bale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:20 Nsanja ya Olonda,9/1/2007, tsa. 3012/1/2006, tsa. 273/15/1988, tsa. 182/1/1987, tsa. 16
20 Ngati wina amanena kuti: “Ndimakonda Mulungu,” koma amadana ndi m’bale wake, ndiye kuti ndi wabodza.+ Pakuti amene sakonda m’bale wake+ amene amamuona, sangakonde Mulungu amene sanamuonepo.+