Chivumbulutso 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe, pali chinthu chimodzi chimene ukuchita bwino: Umadana+ ndi ntchito za mpatuko wa Nikolao,+ zimenenso ine ndimadana nazo. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 35-36 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 11
6 Komabe, pali chinthu chimodzi chimene ukuchita bwino: Umadana+ ndi ntchito za mpatuko wa Nikolao,+ zimenenso ine ndimadana nazo.