Chivumbulutso 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 akulu 24 aja+ anali kugwada ndi kuwerama pamaso pa Wokhala pampando wachifumuyo, ndi kulambira+ wokhala ndi moyo kwamuyayayo. Iwo anali kuponya pansi zisoti zawo zachifumu pamaso pa mpando wachifumuwo, ndi kunena kuti: Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:10 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 81
10 akulu 24 aja+ anali kugwada ndi kuwerama pamaso pa Wokhala pampando wachifumuyo, ndi kulambira+ wokhala ndi moyo kwamuyayayo. Iwo anali kuponya pansi zisoti zawo zachifumu pamaso pa mpando wachifumuwo, ndi kunena kuti: