Chivumbulutso 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dzina la nyenyeziyo ndi Chitsamba Chowawa. Choncho gawo limodzi mwa magawo atatu a madzi linakhala lowawa, ndipo anthu ambiri anafa ndi madziwo chifukwa anali owawa.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:11 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 136-139 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 12
11 Dzina la nyenyeziyo ndi Chitsamba Chowawa. Choncho gawo limodzi mwa magawo atatu a madzi linakhala lowawa, ndipo anthu ambiri anafa ndi madziwo chifukwa anali owawa.+