Chivumbulutso 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo, Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 284-285
17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,