Chivumbulutso 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kum’mawa kwa mzindawo kunali zipata zitatu, kumpoto zipata zitatu, kum’mwera zipata zitatu, ndipo kumadzulo kwake zipata zitatu.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:13 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 302, 306
13 Kum’mawa kwa mzindawo kunali zipata zitatu, kumpoto zipata zitatu, kum’mwera zipata zitatu, ndipo kumadzulo kwake zipata zitatu.+