2 Mtsinjewo unali kudutsa pakati pa msewu waukulu wa mumzindawo. Kumbali iyi ya mtsinjewo ndi kumbali inayo, kunali mitengo+ ya moyo yobala zipatso zokolola maulendo 12, ndipo inali kubala zipatso mwezi uliwonse.+ Masamba a mitengoyo anali ochiritsira mitundu ya anthu.+