Mawu a M'munsi
M’Baibulo lonse, mawu akuti “Ya” akutchulidwa koyamba pavesi lino. Mawu amenewa ndi chidule cha dzina lakuti “Yehova,” ndipo ndi mbali yoyamba ya zilembo zinayi zoimira dzina lenileni la Mulungu, lakuti YHWH. Onani Zakumapeto 2.