Mawu a M'munsi c Zinthu zokongoletsera mkati mwa kachisi wa Solomo ndiponso zipangizo zimene zinali m’kachisimo anazipanga kapena kuzikutira ndi golide, koma zinthu za m’bwalo la kachisiyo zinali zamkuwa.—1 Mafumu 6:19-23, 28-35; 7:15, 16, 27, 30, 38-50; 8:64.