Mawu a M'munsi
b Liwu la Chihebri limene kaŵirikaŵiri limatanthauzidwa kuti “chopereka” ndi qor·banʹ. Polemba za mmene Yesu anatsutsira mkhalidwe wotayirira zinthu wa alembi ndi Afarisi, Marko anafotokoza kuti “korban” amatanthauza kuti “mtulo.”—Marko 7:11.