Mawu a M'munsi
b Onani Nsanja ya Olonda, ya August 1, 1998, tsamba 13, ndime 7. Monga pulogalamu ya kuphunzira Baibulo, mungapende nkhani zonse zophunziridwa m’kope limenelo komanso nkhani zakuti “Justice,” “Mercy,” ndi “Righteousness” mu insaikulopediya ya Baibulo ya Insight on the Scriptures, yofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.