Mawu a M'munsi
a Maphunziro ameneŵa angafanane ndi amene Danieli ndi anzake aja anaphunzira kuti akagwire ntchito za boma ku Babulo. (Danieli 1:3-7) Yerekezani ndi buku la Samalani Ulosi wa Danieli!, mutu 3, lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.